Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Deuteronomo 21:1-2 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

1. Akapeza munthu waphedwa m'dziko limene Yehova Mulungu wanu akupatsani likhale lanu lanu, nagona pamunda, wosadziwika wakumkantha,

2. pamenepo azituruka akuru anu ndi oweruza anu, nayese ku midzi yomzinga wophedwayo;

Werengani mutu wathunthu Deuteronomo 21