Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Deuteronomo 21:1 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Akapeza munthu waphedwa m'dziko limene Yehova Mulungu wanu akupatsani likhale lanu lanu, nagona pamunda, wosadziwika wakumkantha,

Werengani mutu wathunthu Deuteronomo 21

Onani Deuteronomo 21:1 nkhani