Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Deuteronomo 2:25 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Tsiku lino ndiyamba kuopsetsa nawe ndi kucititsa mantha nawe anthu a pansi pa thambo lonse, amene adzamva mbiri yako, nadzanjenjemera, nadzawawidwa cifukwa ca iwe.

Werengani mutu wathunthu Deuteronomo 2

Onani Deuteronomo 2:25 nkhani