Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Deuteronomo 2:24 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Uka, yenda ulendo wako, ndi kuoloka mtsinje wa Arinoni; taonani, ndapereka Sihoni mfumu ya Hesiboni, M-amori, ndi dziko lace m'dzanja lako; yamba kulilandira, ndi kuutsana naye nkhondo.

Werengani mutu wathunthu Deuteronomo 2

Onani Deuteronomo 2:24 nkhani