Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Deuteronomo 2:14 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo masiku amene tinayenda kucokera ku Kadesi Barinea, kufikira tidaoloka mtsinje wa Zeredi, ndiwo zaka makumi atatu mphambu zisanu ndi zitatu; kufikira utatha mbadwo wonse wa amuna ankhondo m'cigono, monga Yehova adawalumbirira.

Werengani mutu wathunthu Deuteronomo 2

Onani Deuteronomo 2:14 nkhani