Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Deuteronomo 19:6 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

kuti wolipsa mwazi angalondole wakupha mnzace, pokhala mtima wace watentha, nampeza, popeza njira njaitali, namkantha kuti wafa; angakhale sanaparamula imfa, poona sanamuda kale lonse.

Werengani mutu wathunthu Deuteronomo 19

Onani Deuteronomo 19:6 nkhani