Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Deuteronomo 19:5 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

monga ngati munthu analowa kunkhalango ndi mnzace kutema mitengo, ndi dzanja lace liyendetsa nkhwangwa kutema mtengo, ndi nkhwangwa iguruka m'mpinimo, nikomana ndi mnzace, nafa nayo; athawire ku wina wa midzi iyi, kuti akhale ndi moyo;

Werengani mutu wathunthu Deuteronomo 19

Onani Deuteronomo 19:5 nkhani