Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Deuteronomo 16:8 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Masiku asanu ndi limodzi muzidya mkate wopanda cotupitsa; ndipo tsiku lacisanu ndi ciwiri ndilo loletsa, la Yehova Mulungu wanu; musamagwira nchito pamenepo.

Werengani mutu wathunthu Deuteronomo 16

Onani Deuteronomo 16:8 nkhani