Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Deuteronomo 16:18 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Mudziikire oweruza ndi akapitao m'inidzi yanu yonse imene Yehova Mulungu wanu akupatsani, monga mwa mapfuko anu; ndipo aweruze anthu ndi ciweruzo colungama.

Werengani mutu wathunthu Deuteronomo 16

Onani Deuteronomo 16:18 nkhani