Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Deuteronomo 16:10 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo mucitire Yehova Mulungu wanu madyerero a masabata, ndiwo msonkho waufulu wa dzanja lanu, umene mupereke monga Yehova Mulungu wanu akudalitsani.

Werengani mutu wathunthu Deuteronomo 16

Onani Deuteronomo 16:10 nkhani