Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Deuteronomo 15:11 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Popeza waumphawi salekana m'dziko, cifukwa cace ndikuuzani ndi kuti, Dzanja lanu mulitansire ndithu mbale wanu, ndi ozunzika anu, ndi aumphawi anu, a m'dziko mwanu.

Werengani mutu wathunthu Deuteronomo 15

Onani Deuteronomo 15:11 nkhani