Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Deuteronomo 14:3-6 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

3. Musamadya conyansa ciri conse,

4. Nyamazi muyenera kumadya ndi izi: ng'ombe, nkhosa, ndi mbuzi,

5. ngondo, ndi nswala ndi mphoyo, ndi mphalapala, ndi ngoma, ndi nyumbu, ndi mbalale.

6. Ndipo nyama iri yonse yogawanika ciboda, nikhala yogawanikadi ciboda, nibzikula, imeneyo muyenera kudya.

Werengani mutu wathunthu Deuteronomo 14