Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Deuteronomo 14:2 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Popeza ndinu mtundu wa anthu opatulikira Yehova Mulungu wanu, ndipo Yehova anakusankhani mukhale mtundu wa anthu wa pa wokha wa iye yekha, mwa mitundu yonse ya anthu okhala pankhope pa dziko lapansi.

Werengani mutu wathunthu Deuteronomo 14

Onani Deuteronomo 14:2 nkhani