Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Deuteronomo 14:23 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo muzidye pamaso pa Yehova Mulungu wanu, m'malo m'mene asankhamo iye, kukhalitsamo dzina lace; limodzi la magawo khumi la tirigu wanu, la vinyo wanu, ndi la mafuta anu, ndi oyamba kubadwa a ng'ombe zanu ndi a nkhosa ndi mbuzi zanu; kuti muphunzire kuopa Yehova Mulungu wanu masiku onse.

Werengani mutu wathunthu Deuteronomo 14

Onani Deuteronomo 14:23 nkhani