Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Deuteronomo 12:7 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

ndipo kumeneko muzidya pamaso pa Yehova Mulungu wanu, ndi kukondwera nazo zonse mudazigwira ndi dzanja lanu, inu ndi a pa banja lanu, m'mene Yehova Mulungu wanu anakudalitsani.

Werengani mutu wathunthu Deuteronomo 12

Onani Deuteronomo 12:7 nkhani