Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Deuteronomo 12:6 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

ndi kubwera nazo kumeneko nsembe zanu zopsereza, ndi nsembe zanu zophera, ndi magawo anu onse a magawo khumi, ndi nsembe yokweza ya dzanja lanu, ndi zowinda zanu, ndi nsembe zanu zaufulu, ndi zoyamba kubadwa za ng'ombe zanu, ndi za nkhosa ndi mbuzi zanu;

Werengani mutu wathunthu Deuteronomo 12

Onani Deuteronomo 12:6 nkhani