Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Deuteronomo 12:21 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Malo amene Yehova Mulungu wanu adzasankha kuikako dzina lace akakutanimphirani, muziphako ng'ombe zanu ndi nkhosa ndi mbuzi zanu zimene Yehova anakupatsani, monga ndinakuuzani, ndi kuzidya m'mudzi mwanu, monga umo monse ukhumba moyo wanu.

Werengani mutu wathunthu Deuteronomo 12

Onani Deuteronomo 12:21 nkhani