Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Deuteronomo 12:20 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Akadzakuza malire a dziko lanu Yehova Mulungu wanu, monga ananena ndi inu, ndipo mukadzati, Ndidye nyama, popeza moyo wanga ukhumba kudya nyama; mudye nyama monga umo monse ukhumba moyo wanu.

Werengani mutu wathunthu Deuteronomo 12

Onani Deuteronomo 12:20 nkhani