Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Deuteronomo 12:18 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

koma muzizidya pamaso pa Yehova Mulungu wanu m'malo amene Yehova Mulungu wanu adzasankha, inu, ndi ana anu amuna, ndi ana anu akazi, ndi anchito anu amuna, ndi anchito anu akazi, ndi Mlevi ali m'mudzi mwanu; nimukondwere pamaso pa Yehova Mulungu wanu m'zonse mudazigwira ndi dzanja lanu.

Werengani mutu wathunthu Deuteronomo 12

Onani Deuteronomo 12:18 nkhani