Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Deuteronomo 12:17 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Simukhoza kudya m'mudzi mwanu limodzi la magawo khumi la tirigu wanu, kapena la vinyo wanu, kapena la mafuta anu, kapena oyambakubadwa a ng'ombe zanu kapena la nkhosa ndi mbuzi zanu, kapena zowinda zanu ziri zonse muzilonieza kapena nsembe zanu zaufulu, kapena nsembe yokweza ya m'dzanja lanu;

Werengani mutu wathunthu Deuteronomo 12

Onani Deuteronomo 12:17 nkhani