Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Deuteronomo 12:15 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Koma monga mwa cikhumbu conse ca moyo wanu muiphe ndi kudya nyama m'midzi yanu yonse, monga mwa mdalitso wa Yehova Mulungu wanu anakupatsani; odetsa ndi oyera adyeko, monga yamphoyo ndi yangondo.

Werengani mutu wathunthu Deuteronomo 12

Onani Deuteronomo 12:15 nkhani