Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Deuteronomo 11:9 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

ndi kuti masiku anu acuruke m'dziko limene Yehova analumbirira makolo anu, kuti adzawapatsa iwo ndi mbeu zao, dziko moyenda mkaka ndi uci ngati madzi.

Werengani mutu wathunthu Deuteronomo 11

Onani Deuteronomo 11:9 nkhani