Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Deuteronomo 11:10 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Pakuti dziko limene mumkako kulilandira ndi losanga dziko la Aigupto lija mudaturukako, kumene kuja munafesa mbeu zanu, ndi kuzithirira ndi phazi lanu, monga munda watherere;

Werengani mutu wathunthu Deuteronomo 11

Onani Deuteronomo 11:10 nkhani