Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Deuteronomo 1:41 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Pamenepo munayankha ndi kunena ndi ine, Tacimwira Yehova, tidzakwera ndi kuthira mkhondo monga mwa zonse Yehova Mulungu wathu atiuza. Ndipo munadzimangira munthu yense zida zace za nkhondo, nimunakonzeka kukwera kumka kumapiri.

Werengani mutu wathunthu Deuteronomo 1

Onani Deuteronomo 1:41 nkhani