Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Danieli 9:24 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Masabata makumi asanu ndi awiri alamulidwira anthu amtundu wako ndi mudzi wako wopatulika, kumariza colakwaco, ndi kutsiriza macimo, ndi kutetezera mphulupulu, ndi kufikitsa cilungamo cosalekeza, ndi kukhomera cizindikilo masomphenya ndi zonenera, ndi kudzoza malo opatulikitsa.

Werengani mutu wathunthu Danieli 9

Onani Danieli 9:24 nkhani