Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Danieli 9:20 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo pakunena ine, ndi kupemphera, ndi kubvomereza cimo langa, ndi cimo la anthu amtundu wanga Israyeli, ndi kutula cipembedzero canga pamaso pa Yehova Mulungu wanga, cifukwa ca phiri lopatulika la Mulungu wanga;

Werengani mutu wathunthu Danieli 9

Onani Danieli 9:20 nkhani