Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Danieli 8:7 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo ndinamuona wayandikira pafupi pa nkhosa yamphongo, nawawidwa mtima nayo, naigunda nkhosa yamphongo, natyola nyanga zace ziwiri; ndipo mphongoyo inalibe mphamvu yakuima pamaso pace, koma anaigwetsa pansi, naipondereza; ndipo panalibe wakupulumutsa mphongoyo m'dzanja lace.

Werengani mutu wathunthu Danieli 8

Onani Danieli 8:7 nkhani