Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Danieli 8:4 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndinaona nkhosa yamphongo irikugunda kumadzulo, ndi kumpoto, ndi kumwela; ndipo panalibe zamoyo zokhoza kuima pamaso pace; panalibenso wakulanditsa m'dzanja lace; koma inacita monga mwa cifuniro cace, nidzikulitsa.

Werengani mutu wathunthu Danieli 8

Onani Danieli 8:4 nkhani