Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Danieli 8:3 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo ndinakweza maso anga ndi kupenya; taonani, panaima pamtsinje nkhosa yamphongo yokhala nazo nyanga ziwiri, ndi nyanga ziwirizo zinali za msinkhu wautali, koma imodzi inaposa inzace; yoposayo inaphuka m'mbuyo.

Werengani mutu wathunthu Danieli 8

Onani Danieli 8:3 nkhani