Ndi mphamvu yace idzakhala yaikuru, koma si mphamvu yace yace ai, nidzaononga modabwiza, nidzakuzika, ndi kucita, ndi kuononga amphamvuwo, ndi anthu opatulikawo.