Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Danieli 8:1-2 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

1. Caka cacitatu ca Belisazara mfumu masomphenya anandionekera kwa ine Danieli, atatha kundionekera oyamba aja.

2. Ndipo ndinaona m'masomphenya; tsono kunali, pakuwaona ine ndinali m'Susani, m'nyumba ya mfumu, ndiwo m'dziko la Elamu; ndinaona m'masomphenya kuti ndinali kumtsinje Ulai.

Werengani mutu wathunthu Danieli 8