Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Danieli 6:27-28 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

27. Iye apulumutsa, nalanditsa, nacita zizindikilo ndi zozizwa m'mwamba ndi pa dziko lapansi, ndiye amene anapulumutsa Danieli ku mphamvu ya mikango.

28. Momwemo Danieli amene anakuzikabe pokhala Dariyo mfumu, ndi pokhala mfumu Koresi wa ku Perisiya.

Werengani mutu wathunthu Danieli 6