Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Danieli 6:16 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Pamenepo inalamula mfumu, ndipo anadza naye Danieli, namponya m'dzenje la mikango. Ndipo mfumu inalankhula, niti kwa Danieli, Mulungu wako amene umtumikira kosalekeza, Iyeyu adzakulanditsa.

Werengani mutu wathunthu Danieli 6

Onani Danieli 6:16 nkhani