Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Danieli 5:2 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Belisazara, pakulawa vinyo, anati abwere nazo zotengera za golidi ndi siliva adazicotsa Nebukadinezara atate wace ku Kacisi ali ku Yerusalemu, kuti mfumu ndi akuru ace, akazi ace ndi akazi ace ang'ono, amweremo.

Werengani mutu wathunthu Danieli 5

Onani Danieli 5:2 nkhani