Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Danieli 4:8 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Koma potsiriza pace analowa pamaso panga Danieli, dzina lace ndiye Belitsazara, monga mwa dzina la mulungu wanga, amenenso muli mzimu wa milungu yoyera m'mtima mwace; ndipo ndinamfotokozera lotoli pamaso pace, ndi kuti,

Werengani mutu wathunthu Danieli 4

Onani Danieli 4:8 nkhani