Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Danieli 4:34 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Atatha masiku awa tsono, ine Nebukadinezara ndinakweza maso anga kumwamba, ndi nzeru zanga zinandibwerera; ndipo ndinalemekeza Wam'mwambamwamba, ndi kumyamika ndi kumcitira ulemu Iye wokhala cikhalire; pakuti kulamulira kwace ndiko kulamulira kosatha, ndi ufumu wace ku mibadwo mibadwo;

Werengani mutu wathunthu Danieli 4

Onani Danieli 4:34 nkhani