Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Danieli 4:32 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Nadzakuinga kukucotsa kwa anthu, ndi pokhala pako udzakhala pamodzi ndi nyama za kuthengo; adzakudyetsa udzu ngati ng'ombe; nizidzakupitira nthawi zisanu ndi ziwiri, mpaka udzadziwa kuti Wam'mwambamwamba alamulira m'ufumu wa anthu, naupereka kwa ali yense Iye afuna mwini.

Werengani mutu wathunthu Danieli 4

Onani Danieli 4:32 nkhani