Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Danieli 3:7 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Potero nthawi yomweyo pakumva anthu onse mau a lipenga, citoliro, zeze, sansi, cisakasa, ndi zoyimbitsa ziri zonse, anthu onse, mitundu ya anthu a manenedwe osiyana, anagwadira, nalambira fano lagolidi adaliimika mfumu Nebukadinezara.

Werengani mutu wathunthu Danieli 3

Onani Danieli 3:7 nkhani