Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Danieli 3:28 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Nebukadinezara ananena, nati, Alemekezedwe Mulungu wa Sadrake, Mesake, ndi Abedinego, amene anatuma mthenga wace, napulumutsa atumiki ace omkhulupirira Iye, nasanduliza mau a ine mfumu, napereka matupi ao kuti asatumikire kapena kulambira mulungu wina yense, koma Mulungu wao wao.

Werengani mutu wathunthu Danieli 3

Onani Danieli 3:28 nkhani