Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Danieli 3:27 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo akalonga, akazembe, ndi ziwanga, ndi mandoda a mfumu, atasonkhana, anaona amuna awa, kuti moto unalibe mphamvu pa matupi ao, losawauka tsitsi la pamutu pao, ndi zopfunda zao zosasandulika, pfungo lomwe lamoto losawaomba.

Werengani mutu wathunthu Danieli 3

Onani Danieli 3:27 nkhani