Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Danieli 2:41 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo umo mudaonera mapazi ndi zala zace, mwina dongo la woumba, mwina citsulo; ufumuwo udzakhala wogawanika, koma momwemo mudzakhala mphamvu ya citsulo; popeza mudaona citsulo cosanganizika ndi dongo.

Werengani mutu wathunthu Danieli 2

Onani Danieli 2:41 nkhani