Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Danieli 2:29 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Inu mfumu, maganizo anu analowa m'mtima mwanu muli pakama panu, akunena za ico cidzacitika m'tsogolomo; ndipo Iye amene abvumbulutsa zinsinsi wakudziwitsani codzacitikaco.

Werengani mutu wathunthu Danieli 2

Onani Danieli 2:29 nkhani