Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Danieli 2:28 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

koma kuli Mulungu Kumwamba wakubvumbulutsa zinsinsi; Iye ndiye wadziwitsa mfumu Nebukadinezara cimene cidzacitika masiku otsiriza. Loto lanu, ndi masomphenya a m'mtima mwanu pakama panu, ndi awa:

Werengani mutu wathunthu Danieli 2

Onani Danieli 2:28 nkhani