Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Danieli 11:2 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo tsopano ndikufotokozera coonadi. Taona, adzaukanso mafumu atatu m'Perisiya, ndi yacinai idzakhala yoletnera ndithu yoposa onsewo; ndipo itadzilimbitsa yokha mwa kulemera kwace idzawautsa onse alimbane nao ufumu wa Helene.

Werengani mutu wathunthu Danieli 11

Onani Danieli 11:2 nkhani