Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Danieli 10:11 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Nati kwa ine, Danieli, munthu wokondedwatu iwe, tazindikira mau ndirikunena ndi iwe, nukhale ciriri; pakuti ndatumidwa kwa iwe tsopano. Ndipo pamene adanena mau awa kwa ine ndinaimirira ndi kunjenjemera.

Werengani mutu wathunthu Danieli 10

Onani Danieli 10:11 nkhani