Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Danieli 1:10 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Nati mkuru wa adindo kwa Danieli. Ine ndiopa mbuyanga mfumu, amene anakuikirani cakudya canu ndi cakumwa canu; pakuti aonerenji nkhope zanu zacisoni zoposa za anyamata olingana ndi inu? momwemo mudzaparamulitsa mutu wanga kwa mfumu.

Werengani mutu wathunthu Danieli 1

Onani Danieli 1:10 nkhani