Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Amosi 9:14 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo ndidzabwezanso undende wa anthu anga Israyeli, ndipo adzamanganso mabwinja, ndi kukhala m'menemo; nadzaoka minda ya mipesa nadzamwa vinyo wace, nadzalima minda ndi kudya zipatso zace.

Werengani mutu wathunthu Amosi 9

Onani Amosi 9:14 nkhani