Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Amosi 8:10 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo ndidzasanduliza madyerero anu, akhale maliro, ndi nyimbo zanu zikhale za maliro, ndi kufikitsa ziguduli m'cuuno monse, ndi mpala pa mutu uli wonse; nadzakhala ngati maliro a mwana mmodzi yekha, ndi citsiriziro cace ngati tsiku lowawa.

Werengani mutu wathunthu Amosi 8

Onani Amosi 8:10 nkhani