Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Amosi 5:11 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Popeza tsono mupondereza aumphawi, ndi kumsonkhetsa tirigu; mwamanga nyumba za miyala yosema, koma simudzakhala m'mwemo; mwaoka minda ya mipesa yokonda, koma simudzamwa vinyo wace.

Werengani mutu wathunthu Amosi 5

Onani Amosi 5:11 nkhani