Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Amosi 1:13 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Atero Yehova, Cifukwa ca zolakwa zitatu za ana a Amoni, kapena zinai, sindidzabweza kulanga kwace; popeza anatumbula akazi ali m'pakati a Gileadi, kuti akuze malire ao;

Werengani mutu wathunthu Amosi 1

Onani Amosi 1:13 nkhani